Mawu a M'munsi
b Nkhani ino ikufotokoza kufunika kokambirana ndi ana anu nkhani zokhudza kugonana ndi cholinga chowateteza kuti wina asawaphunzitse zinthu zoipa pa nkhani imeneyi. Magazini ina m’tsogolo muno idzafotokoza mmene makolo angaperekere malangizo abwino pokambirana ndi ana awo za kugonana.