Mawu a M'munsi
a Baibulo lachigiriki lotchedwa Chipangano Chatsopano m’Chigiriki Choyambirira [The New Testament in the Original Greek], lomasuliridwa ndi Westcott ndi Hort ndi limene analigwiritsa ntchito pomasulira Malemba Achigiriki. Pomasulira Malemba Achiheberi anagwiritsa ntchito Baibulo lachiheberi lomasuliridwa ndi R. Kittel lotchedwa Baibulo Lachiheberi [Biblia Hebraica].