a Chochititsa chidwi n’chakuti, patapita zaka 1,000 kuchokera pamene Davide anamwalira, gulu la angelo linaonekera kwa abusa n’kuwauza za kubadwa kwa Mesiya. Pa nthawiyi, abusawa ankayang’anira nkhosa kutchire pafupi ndi Betelehemu.—Luka 2:4, 8, 13, 14.