Mawu a M'munsi
b Mfundo imeneyi ndi yosiyana ndi zimene Baibulo limaphunzitsa chifukwa Baibulo limaphunzitsa kuti zonse zimene Mulungu analenga zinali zabwino. Limafotokozanso kuti pali wina amene anayambitsa zoipa. (Deuteronomo 32:4, 5) Yehova atamaliza kulenga zinthu padziko lapansi ananena kuti zonse zimene analengazo “zinali zabwino kwambiri.”—Genesis 1:31.