Mawu a M'munsi
a A Mboni za Yehova atulutsa mabuku ndi zinthu zosiyanasiyana zothandiza kuphunzira komanso kufufuza nkhani za m’Baibulo. Zinthu zimenezi zingakuthandizeni kuti mupindule powerenga Baibulo. Ngati mukufuna kupeza zinthu zimenezi, funsani a Mboni za Yehova.