Mawu a M'munsi
a Koma mwina tsiku limeneli silingafanane ndi limene Ayuda amachita Pasika masiku ano. N’chifukwa chiyani zili choncho? Ayuda ambiri masiku ano amachita Pasika pa Nisani 15 chifukwa amakhulupirira kuti lamulo la pa Ekisodo 12:6 linkanena kuti azichita Pasika pa Nisani 15. (Werengani Nsanja ya Olonda ya February 15, 1990, tsamba 14.) Kuti mudziwe zambiri zokhudza mmene mungawerengere masiku kuti mupeze tsiku limeneli, werengani Nsanja ya Olonda yachingerezi ya June 15, 1977, tsamba 383 mpaka 384.