Mawu a M'munsi
d Manambalawa akusonyeza mitu ya m’buku lakuti Munthu Wamkulu Woposa Onse Amene Anakhalako (gt). Mungaone tchati chosonyeza tsatanetsatane wa zimene Yesu anachita masiku ake omaliza kuchita utumiki, mu buku lachingelezi la “All Scripture Is Inspired of God and Beneficial,” tsamba 290. Mabuku amenewa ndi ofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.