Mawu a M'munsi
a Dzina la mneneri wochokera ku Nazareti ameneyu lakuti “Yesu” limatanthauza “Yehova Ndiye Chipulumutso.” Mawu akuti “Khristu” amatanthauza “Wodzozedwa.” Zimenezi zikusonyeza kuti Yesu anadzozedwa kapena kuti anapatsidwa udindo wapadera ndi Mulungu.