Mawu a M'munsi
a Kuti mudziwe zambiri za Ufumu wa Mulungu komanso chifukwa chake tikunena kuti ubwera posachedwa, werengani mutu 8 wakuti “Kodi Ufumu wa Mulungu N’chiyani” ndi mutu 9 woti “Kodi Tili ‘M’masiku Otsiriza’?,” m’buku la Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.