Mawu a M'munsi a Kuti mudziwe zambiri za zimene Baibulo limaphunzitsa pa nkhani yakuti akufa adzauka, werengani mutu 7 m’buku la Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.