Mawu a M'munsi
a Palembali, mawu amene anawamasulira kuti “dipo” akutanthauza “kuphimba.” (Yobu 33:24; mawu am’munsi) Pa nkhani ya Yobu, dipo liyenera kuti inali nsembe ya nyama imene Mulungu anailandira kuti iphimbe kapena kuti kulipira machimo a Yobu.—Yobu 1:5.