Mawu a M'munsi
a Kuti mudziwe zambiri zokhudza ulosi wa m’Baibulo umene umasonyeza kuti chaka cha 1914 ndi chimene Yesu anakhala Mfumu, werengani tsamba 215 mpaka 218 m’buku lakuti Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? Buku limeneli ndi lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.