Mawu a M'munsi
b Chitsanzo cha nkhani zonama zimene zinalipo m’nthawi ya Paulo ndi buku la Tobit (kapena kuti Tobias) limene anthu ena amaganiza kuti ndi mbali ya Baibulo. Bukuli linalembedwa zaka za m’ma 200 B.C.E. ndipo lili ndi nkhani zambiri zabodza ndiponso zamatsenga. Nkhani zake zimakhala zoti sizingachitike koma m’bukuli anazilemba ngati kuti ndi zoona.—Insight on the Scriptures, Voliyumu 1, tsamba 122.