Mawu a M'munsi
b Pophunzitsa ana aang’ono, makolo angagwiritse ntchito buku lakuti, Phunzirani kwa Mphunzitsi Waluso limene limafotokoza kwambiri zimene Yesu Khristu anaphunzitsa, kapena lakuti Bukhu Langa la Nkhani za Baibulo limene limafotokoza mfundo zikuluzikulu za m’Baibulo m’njira yosavuta. Pophunzitsa achinyamata, makolo angagwiritse ntchito mabuku akuti, Mayankho a Zimene Achinyamata Amafunsa—Buku Loyamba ndi Lachiwiri.