Mawu a M'munsi
b Dzina lake lenileni linali Louys Robert, koma anasintha kuti dzina lake loyamba likhale Pierre. Zikuoneka kuti anamupatsa dzina lakuti Olivétan chifukwa chakuti ankagwiritsa ntchito mafuta ambiri a maolivi munyali zimene ankaunikira usiku pogwira ntchito yake.