Mawu a M'munsi
a Padziko lonse, a Mboni za Yehova amaphunzitsa anthu Baibulo panyumba pawo kwaulere ngati anthuwo akufuna kumvetsa bwino Baibulo. Ngati mukufuna kuphunzira Baibulo, uzani a Mboni za Yehova akwanuko kapena lemberani ku adiresi yoyenera pa maadiresi amene ali patsamba 4.