Mawu a M'munsi
a Mawu akuti por·neiʹa, angatanthauzenso chigololo, kugonana kwa amuna kapena akazi okhaokha komanso kugona nyama. Zinthu zimenezi n’zosagwirizana ndi cholinga cha Mulungu polenga anthu.