Mawu a M'munsi
b Kuti mudziwe zambiri zokhudza mfundo zothandiza za m’Baibulo, kambiranani ndi Mboni za Yehova za m’dera lanu. Kapena lembani kalata pogwiritsa ntchito adiresi yoyenera pa maadiresi amene ali patsamba 4. Kapenanso mungapite pamalo athu a pa Intaneti pogwiritsa ntchito adiresi iyi: www.jw.org.