Mawu a M'munsi
a Poyamba, Abulahamu ankatchedwa Abulamu ndipo mkazi wake ankatchedwa Sarai. Kenako Mulungu anasintha dzina la Abulamu kukhala Abulahamu, kutanthauza “Tate wa Khamu la Anthu” komanso dzina la Sarai kukhala Sara, kutanthauza “Mfumukazi.” (Genesis 17:5, 15) Koma mu nkhanizi tizingowatchula kuti Abulahamu ndi Sara.