Mawu a M'munsi
a Baibulo siliphunzitsa kuti Mulungu anabereka Yesu kudzera mwa mkazi. M’malomwake Yehova analenga munthu wauzimu ameneyu, yemwe patapita nthawi anamutumiza padziko lapansi ndipo anabadwa kwa namwali wotchedwa Mariya. Choncho popeza kuti Mulungu ndi amene analenga Yesu, mpake kuti iye amatchedwa Atate wa Yesu.