Mawu a M'munsi
a Anthu ambiri amagwiritsa ntchito dzina la malo ponena za nkhondo. Mwachitsanzo, mzinda wina wa ku Japan wotchedwa Hiroshima, womwe unawonongedwa ndi bomba, panopa umaonedwa ngati chizindikiro chakuti nkhondo ya zida zoopsa ikhoza kuyambika.