Mawu a M'munsi
b Malangizo a Paulo saletsa anthu kupatukana mogwirizana ndi malamulo a boma ngati pali mavuto aakulu kwambiri. Aliyense ayenera kusankha yekha zochita pa nkhani imeneyi. Onani buku lakuti “Khalanibe M’chikondi cha Mulungu,” tsamba 220 mpaka 221.