Mawu a M'munsi
a Chinawato chili m’gulu la chinenero chinachake chotchedwa Uto-Aztec chimene chimalankhulidwa ndi Ahopi, Ashoshone ndi Akomanche a ku North America. Mawu ena achingelezi monga avocado, chocolate, coyote, ndi tomato anachoka m’chinenero cha Chinawato.