Mawu a M'munsi
a Zaka zambiri izi zisanachitike, mu 997 B.C.E., Aisiraeli anagawikana n’kukhala maufumu awiri. Ufumu wina unali wakum’mwera wa mafuko awiri wa Yuda. Wachiwiri unali wakumpoto wa mafuko 10 ndipo unkatchedwa Efuraimu, chifukwa fuko limeneli ndi limene linali lalikulu.