Mawu a M'munsi
c Baibulo limasonyeza momveka bwino kuti Yesu sanachite chozizwitsa chilichonse mpaka pamene anabatizidwa. (Yohane 2:1-11) Kuti mudziwe zambiri za mabuku owonjezera amene anthu ena amati ali m’gulu la Mauthenga Abwino a m’Baibulo, werengani nkhani imene ili patsamba 18 yakuti, “Kodi Pali Mabuku Ena a Uthenga Wabwino Amene Amafotokoza Nkhani za Yesu Zimene M’Baibulo Mulibe?”