Mawu a M'munsi
c Ngati nthawi zina zingakhale zovuta kusiyiratu kulankhulana ndi munthu amene munachita naye chigololoyo, mwachitsanzo ngati ndi wogwira naye ntchito, muyenera kumalankhulana naye pa zinthu zokhudza ntchito zokha basi. Zingakhalenso bwino kuti muzilankhula ndi munthuyo pagulu ndipo mkazi kapena mwamuna wanu azidziwa zimenezo.