Mawu a M'munsi
a Mchimwene wa Elva dzina lake Frank Lambert anadzakhala mpainiya wakhama kumadera akumidzi m’dziko la Australia. Buku lakuti Yearbook of Jehovah’s Witnesses la 1983, tsamba 110 mpaka 112, limafotokoza zinthu zosangalatsa zimene zinamuchitikira pamene anali kulalikira kumeneko.