Mawu a M'munsi
b Kabuku kakuti Buku la Anthu Onse ndiponso buku lakuti Baibulo—Kodi Ndilo Mawu a Mulungu Kapena a Munthu? omwe ndi ofalitsidwa ndi Mboni za Yehova analembedwa n’cholinga chokuthandizani kudziwa umboni wakuti Baibulo linauziridwa ndi Mulungu.