Mawu a M'munsi
a Lonjezo la Mulungu lonena za “mbewu” ya Davide yodzabadwa m’tsogolo, imene idzatenge mpando wachifumu, linaperekedwa Abisalomu atabadwa kale. Choncho Abisalomu anayenera kudziwa kuti sanasankhidwe ndi Yehova kuti alowe ufumu wa Davide.—2 Sam. 3:3; 7:12.