Mawu a M'munsi
a Sikuti Danieli anaona Mulungu. Koma Mulunguyo anangomuonetsa masomphenya m’maganizo mwake. Pofotokoza zimene anaona m’masomphenyawo, Danieli anagwiritsa ntchito mawu ophiphiritsa komanso oyerekezera omwe amam’fotokoza Mulungu ngati munthu. Kafotokozedwe kameneka kamangotithandiza kumvetsa mmene Mulungu alili koma sizikutanthauza kuti iye amaoneka ngati munthu.