Mawu a M'munsi
b Nkhani za anthu 8 amenewa zimapezeka pa 1 Mafumu 17:17-24; 2 Mafumu 4:32-37; 13:20, 21; Luka 7:11-17; 8:40-56; Yohane 11:38-44 ndi Machitidwe 9:36-42; 20:7-12. Mukamawerenga nkhani zimenezi, muona kuti panali anthu amene anaona anthuwa akuukitsidwa. Munthu wa 9 amene anaukitsidwa anali Yesu Khristu.—Yohane 20:1-18.