Mawu a M'munsi
a Mauthenga amenewa ankawapatsa mayina potengera munthu amene akuona kuti anamvetsa bwino mfundo inayake imene Yesu anaphunzitsa. Zitsanzo za Mauthenga oterewa ndi ngati umene amati Uthenga Wabwino wa Tomasi komanso umene amati Uthenga Wabwino wa Mariya Mmagadala. Mauthenga Abwino oterewa alipo 30.