Mawu a M'munsi
b Akatswiri amene amanena kuti Yudasi anali chiwanda, chimene chinkadziwa bwino Yesu kuposa ophunzira enawo, amaona kuti izi n’zofanana ndi zimene ziwanda zotchulidwa mu Uthenga Wabwino weniweni wa m’Baibulo zinkachita. Izo zinanena molondola zokhudza Yesu.—Maliko 3:11; 5:7.