Mawu a M'munsi
a M’Baibulo, mawu achigiriki amene anawamasulira kuti “kuuka” amatanthauza “kuimiranso.” Amatanthauza kuti moyo wa munthu wabwezeretsedwa ndipo munthuyo ali mmene analili poyamba komanso akukumbukira zonse zimene ankadziwa.