Mawu a M'munsi a Dzina la Mulungu ndi lochokera ku verebu lachiheberi limene limatanthauza “kukhala.” Choncho dzina lakuti Yehova limatanthauza kuti “Iye Amachititsa Kukhala.”—Gen. 2:4, (Onani Zakumapeto 1 ndime 1 m’Baibulo la Dziko Latsopano.)