Mawu a M'munsi
a Pa nthawi imeneyo anthu ankakhala zaka zambirimbiri kuposa masiku ano. Ziyenera kuti zinali choncho chifukwa panali pasanapite nthawi yaitali kuchokera pamene Adamu ndi Hava anakhala opanda ungwiro.