Mawu a M'munsi
b Lameki anapatsa mwana wake dzina loti Nowa lomwe mwina limatanthauza “Mpumulo.” Iye analoseranso kuti Nowa adzakwaniritsa tanthauzo la dzina lake pothandiza kuti temberero la nthaka lichotsedwe. (Genesis 5:28, 29) Koma Lameki anamwalira ulosi umenewu usanakwaniritsidwe.