Mawu a M'munsi
a Pali madokotala anayi amene anatulukira matendawa. Choncho amatchedwa matenda a Laurence-Moon-Bardet-Biedl potengera mayina a madokotalawo. Munthu amachita kubadwa nawo matendawa ndipo alibe mankhwala. Masiku ano anthu amangowatchula kuti matenda a Bardet-Biedl.