Mawu a M'munsi
a Kuti mupeze malangizo ena, onani nkhani yakuti “Kodi Mwalimbikitsapo Aliyense Posachedwapa?” mu Nsanja ya Olonda ya January 15, 1995 ndiponso yakuti “Fulumizanani ku Chikondano ndi Ntchito Zabwino—Motani?” mu Nsanja ya Olonda ya April 1, 1995.