Mawu a M'munsi
b Mavuto amene anthu amakumana nawo akakwatira kapena kukwatiwanso amakhala osiyanasiyana mogwirizana ndi mmene banja lawo loyamba linathera. Nkhani ino ithandiza kwambiri anthu amene anakwatira kapena kukwatiwanso banja lawo litatha pazifukwa zomveka kapena amene mwamuna kapena mkazi wawo anamwalira.