Mawu a M'munsi
a Malemba ena m’Baibulo amanena kuti “dziko” ndi lochimwa ndipo lifunika mpulumutsi, zomwe zikusonyeza kuti nthawi zina mawu akuti dziko amatanthauza anthu osati dziko lapansili.—Yohane 1:29; 4:42; 12:47.