Mawu a M'munsi
a Mfundo zimene anthu amanena zokhudza zinenero nthawi zambiri zimatsatira maganizo akuti anthu anachokera ku anyani. Kuti mudziwe zoona zake pa maganizo amenewa onani kabuku kachingelezi kakuti The Origin of LifeāFive Questions Worth Asking, kofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.