Mawu a M'munsi
a Kuti mudziwe zambiri zokhudza zimene Ufumu wa Mulungu udzachite pokwaniritsa cholinga cha Mulungu padziko lapansi, werengani mutu 8 m’buku lakuti, Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova. Mungathenso kuchita dawunilodi bukuli pa webusaiti yathu ya www.pr418.com.