Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO

Mawu a M'munsi

a Pa Machitidwe 20:29, 30, Paulo ananena kuti mumpingo wachikhristu mudzapezeka anthu ena amene “adzayamba kulankhula zinthu zopotoka kuti apatutse ophunzira aziwatsatira.” Izi n’zimene zinachitikadi patapita nthawi chifukwa anthu mumpingo anayamba kugawikana m’magulu awiri. Ena anali atsogoleri pomwe ena anali anthu wamba. Pofika zaka za m’ma 200 C.E., “munthu wosamvera malamulo” anali ataonekera monga atsogoleri a matchalitchi amene amati ndi achikhristu.—Onani Nsanja ya Olonda ya February 1, 1990, tsamba 10 mpaka 14.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena