Mawu a M'munsi
b Naboti ataphedwa, n’kutheka kuti Yezebeli anaganiza kuti mundawo upita kwa ana ake, choncho mwina anakonzanso kuti ana aamuna a Naboti aphedwenso. Kuti mudziwe chifukwa chake Mulungu amalola kuti anthu osauka aziponderezedwa, werengani nkhani yakuti “Zimene Owerenga Amafunsa” patsamba 11.