Mawu a M'munsi
a Ngati tikufuna kuti Mulungu aziyankha mapemphero athu, tiyenera kuyesetsa kuchita zimene iye amafuna. Tikamachita zimenezi, tidzaona kuti pemphero lingatithandizedi monga mmene tionere m’nkhani ino. Kuti mudziwe zambiri, werengani mutu 17 m’buku lakuti, Kodi Baibulo Limaphunzitsa Chiyani Kwenikweni? lofalitsidwa ndi Mboni za Yehova.