Mawu a M'munsi
a Onani nkhani zakuti “Akristu Amalambira Mumzimu ndi M’choonadi” ndiponso yakuti “Amayendabe M’choonadi” mu Nsanja ya Olonda ya July 15, 2002. Mbiri ya mbali ya padziko lapansi ya gulu la Yehova masiku ano yafotokozedwa mwatsatanetsatane m’buku lakuti Jehovah’s Witnesses—Proclaimers of God’s Kingdom.