Mawu a M'munsi
a Mfundo zimenezi ndi monga, kuphunzitsa anthu za kuopsa kosuta, kuletsa kuti fodya asamagulitsidwe mwachisawawa, kukweza msonkho wa fodya komanso kukhazikitsa mapulogalamu othandiza anthu kusiya kusuta.