Mawu a M'munsi
a M’nkhaniyi mawu akuti kusuta, akunena za kulowetsa utsi wa fodya m’mapapo kudzera mu ndudu, fodya wopichira, kaliwo komanso kugwiritsa ntchito chipangizo chimene chimachititsa kuti utsi wa fodya uzidutsa m’madzi, usanalowe m’thupi. Komabe mfundo zomwe zili m’nkhaniyi zikukhudzanso fodya wotafuna, wofwenkha ndi wina wotero.