Mawu a M'munsi
b Kalelo mwamuna akamwalira opanda mwana wamwamuna, m’bale wake ankachita chokolo kapena kuti ukwati wa pachilamu. Ankachita zimenezi n’cholinga choti abereke mwana wamwamuna woti apitirize dzina la m’bale wakeyo.—Gen. 38:8; Deut. 25:5, 6.